Mawu a M'munsi
c MAWU OFOTOKOZERA ZITHUNZI: Poyamba woyang’anira kagulu ka utumiki ankaganiza kuti mlongo wina sakonda kucheza ndi ena koma kenako anamva kuti mlongoyo ndi wamanyazi ndipo amavutika kumasuka ndi anthu amene sawadziwa bwino.