Mawu a M'munsi
a Panopa tikuona umboni woti ulosi wa Danieli wonena za “mfumu ya kumpoto” ndi “mfumu ya kum’mwera,” ukupitiriza kukwaniritsidwa. N’chifukwa chiyani tikutsimikiza chonchi? Nanga n’chifukwa chiyani tiyenera kumvetsa bwino ulosiwu?