Mawu a M'munsi
b Zimene tafotokoza mundimeyi zikusonyeza kuti sitinganenenso kuti mfumu ya Roma dzina lake Aurelian (yemwe analamulira kuyambira mu 270 kufika mu 275 C.E.) ndi amene anali “mfumu ya kumpoto” komanso kuti mfumukazi Zenobia (yemwe analamulira kuyambira mu 267 kufika mu 272 C.E.) ndi amene anali “mfumu ya kum’mwera.” Izi zikusintha zomwe zinafotokozedwa m’mutu 13 ndi 14 wa buku lakuti Samalani Ulosi wa Danieli!