Mawu a M'munsi
e Anthuwo anathandizira kuti boma la Germany ligwe mwansanga m’njira zambiri. Mwachitsanzo, iwo anayamba kuulula zinsinsi za nkhondo, anasiya kuthandiza mfumu komanso anaikakamiza kutula pansi udindo.