Mawu a M'munsi
a Kodi “mfumu ya kumpoto” ndi ndani masiku ano, nanga idzafika bwanji kumapeto a moyo wake? Kudziwa mayankho a mafunsowa kungalimbitse chikhulupiriro chathu komanso kungatithandize kukonzekera mayesero omwe tidzakumane nawo m’tsogolomu.