Mawu a M'munsi
a Kodi n’chifukwa chiyani anthu ena omwe akhala akutumikira Yehova mokhulupirika kwa zaka zambiri, amafooka kapenanso kusiya kumutumikira? Kodi Mulungu amawaona bwanji anthuwa? Nkhaniyi iyankha mafunso amenewa. Itithandizanso kuona mmene Yehova anathandizira anthu ena akale omwe nthawi ina sanachite zimene anawauza.