Mawu a M'munsi
b TANTHAUZO LA MAWU ENA: Wofalitsa amaonedwa kuti ndi wofooka ngati sanapereke malipoti ake autumiki kwa miyezi 6 kapena kuposerapo. Komabe anthu amenewa timawaonabe kuti ndi abale ndi alongo athu ndipo timawakonda kwambiri.