Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

b M’mbuyomu, m’mabuku athu tinkafotokoza kuti dzina la Yehova silifunika kutsimikiziridwa kuti ndi loyera chifukwa palibe amene anatsutsapo kuti Yehova siwoyenera kukhala ndi dzina limeneli. Koma pamsonkhano wapachaka wa 2017, panakambidwa nkhani imene inasintha kafotokozedwe ka mfundo imeneyi. Tcheyamani ananena kuti: “Sikulakwa kunena kuti timapempherera kuti dzina la Yehova litsimikiziridwe kuti ndi loyera chifukwa mbiri yake ikufunika kuti iyeretsedwe.”​—Onani JW Broadcasting ya January 2018 pa jw.org®. Pitani pa LIBRARY > JW BROADCASTING®.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena