Mawu a M'munsi
b TANTHAUZO LA MAWU ENA: Kukhala wofunika mumpingo wa Yehova kukutanthauza zimene aliyense angachite kuti azilimbikitsa abale ndi alongo mumpingo. Zimenezi sizidalira mtundu wathu, ndalama zimene tili nazo, banja limene timachokera, chikhalidwe chathu kapena maphunziro amene tinachita.