Mawu a M'munsi
a Ophunzira Baibulo omwe akusintha moyo wawo, analimbikitsidwa munkhani yapita ija kuti ayambe kulalikira uthenga wabwino. Munkhaniyi tikambirana zinthu zitatu zomwe zingathandize ofalitsa onse, atsopano komanso akale, kuti apitirizebe kugwira ntchito yolalikira uthenga wabwino, mpaka Yehova atanena kuti ntchitoyi yafika kumapeto.