Mawu a M'munsi
a Kodi mumakhala mādziko lomwe mumatha kulambira Yehova mwaufulu? Ngati ndi choncho, kodi mukuigwiritsa ntchito bwanji nthawi ya mtendereyi? Nkhaniyi ikuthandizani kuona zomwe mungachite kuti muzitsanzira Asa yemwe anali Mfumu ya Yuda komanso Akhristu a munthawi ya atumwi. Anthu amenewa anachita zinthu mwanzeru pa nthawi imene zinthu zinali bwino.