Mawu a M'munsi
b TANTHAUZO LA MAWU ENA: Mawu akuti “mtendere” sakungotanthauza nthawi imene kulibe nkhondo. Mawu a Chiheberi omwe anamasuliridwa kuti mtendere amatanthauzanso kukhala ndi thanzi, chitetezo komanso moyo wabwino.