Mawu a M'munsi
a Makolo a Chikhristu amafuna kuti ana awo akadzakula azidzasangalala kutumikira Yehova. Kodi makolo angasankhe kuchita chiyani kuti athandize ana awo kutumikira Yehova? Nanga achinyamata angachite chiyani kuti zinthu ziwayendere bwino pa moyo wawo? Nkhaniyi iyankha mafunso amenewa.