Mawu a M'munsi
a Yesu anauza otsatira ake kuti aziphunzitsa anthu kuti akhale ophunzira ake komanso kuti aziwaphunzitsa kusunga zinthu zonse zimene anawalamula. Munkhaniyi tikambirana zimene tingachite kuti tizitsatira malangizo a Yesuwa. Mfundo zina za munkhaniyi zachokera mu Nsanja ya Olonda ya July 1, 2004, tsamba 14-19.