Mawu a M'munsi
d MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: Mlongo amene anafooka kwa kanthawi akuganizira zimene wakhala akuchita m’mbuyomu potumikira Mulungu ndipo kenako akupemphera kwa Yehova. Sakukayikira kuti Mulungu akukumbukira zimene iye anachita m’mbuyomu komanso zimene akuchita panopa.