Mawu a M'munsi
b MATANTHAUZO A MAWU ENA: Nkhosa zina ndi anthu omwe amatsatira Khristu ndipo akuyembekezera kudzakhala ndi moyo wosatha padzikoli. Ena mwa anthu amenewa anayamba kutumikira Mulungu m’masiku otsiriza. Khamu lalikulu ndi a nkhosa zina amene adzakhale ndi moyo pa nthawi imene Khristu azidzaweruza anthu pa chisautso chachikulu. Ndipo anthu amenewa adzapulumuka pa chisautso chachikulucho.