Mawu a M'munsi
b MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: Mwamuna yemwe ndi mutu wa banja komanso amakhala wotanganidwa, akugwira nawo ntchito yothandiza pakachitika ngozi, akupereka ndalama zothandiza pa Ntchito Yapadziko Lonse komanso waitana ena kuti adzakhale nawo pa kulambira kwawo kwa pabanja.