Mawu a M'munsi
a Ngakhale kuti Chitchainizi ndi chilankhulo chachikulu mādziko la Taiwan, Chijapanizi ndi chomwe chinali chilankhulo chachikulu kwa zaka zambiri. Choncho anthu a zikhalidwe zambiri ku Taiwan ankalankhulanso Chijapanizi.