Mawu a M'munsi
a Abale achinyamata akayamba kukhala pa ubwenzi wabwino ndi Yehova amafuna kuchita zambiri pomutumikira. Ndipo kuti ayenerere kukhala atumiki othandiza, amafunika kumachita zinthu zimene zingachititse kuti anthu ena mumpingo aziwalemekeza. Ndiye kodi angatani kuti ena aziwalemekeza?