Mawu a M'munsi
b Pa nthawi ya utumiki wake, si nthawi zonse pamene Yesu ankalankhula kapena kupereka funso pofuna kusonyeza mmene ankamvera. Nthawi zambiri ankachita zimenezi pofuna kuthandiza ophunzira ake kuti afotokoze maganizo awo.—Maliko 7:24-27; Yoh. 6:1-5; onani Nsanja ya Olonda, ya October 15, 2010, tsamba 4-5.