Mawu a M'munsi
a Abale ndi alongo ena zimawavuta kukhulupirira kuti Yehova amawakonda. Munkhaniyi tikambirana chifukwa chake sitiyenera kukayikira kuti Yehova amatikonda aliyense payekha. Tikambirananso zimene tingachite ngati tayamba kukayikira kuti Mulungu amatikonda.