Mawu a M'munsi
c MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: Poyamba Paulo ankazunza Akhristu n’kumawatsekera m’ndende. Koma atavomereza mumtima mwake zimene Yesu anamuchitira, iye anasintha n’kuyamba kulimbikitsa abale ake a Chikhristu omwe ena mwa iwo anali achibale a anthu omwe anawazunza.