Mawu a M'munsi
a Ngakhale kuti Yesu anali Mphunzitsi wamkulu kuposa onse amene anakhalako, anthu ambiri m’nthawi yake anamukana. N’chifukwa chiyani? Munkhaniyi, tikambirana zifukwa 4. Tikambirananso chifukwa chake anthu ambiri masiku ano sakhulupirira zimene otsatira enieni a Yesu amanena komanso kuchita. Ndipo tiphunziranso chifukwa chake tiyenera kukhulupirira kwambiri Yesu kuti tisakhumudwe n’kusiya kumutsatira.