Mawu a M'munsi
a Munkhaniyi tikambirana mmene Yesu anathandizira anthu kuti akhale ophunzira ake komanso zimene tingachite kuti timutsanzire. Tikambirananso zinthu zina zimene zili m’buku latsopano lakuti, Mungakhale ndi Moyo Mpaka Kalekale. Bukuli lakonzedwa kuti lizithandiza ophunzira Baibulo kupita patsogolo mpaka kufika pobatizidwa.