Mawu a M'munsi
b MATANTHAUZO A MAWU ENA: Munkhaniyi kunyada kukutanthauza kudziona kukhala wabwino kwambiri kuposa ena. Ndipo dyera likutanthauza kulakalaka kukhala ndi ndalama kapena mphamvu zambiri, kumangokhala ndi chilakolako chofuna kugonana komanso zinthu zina ngati zimenezi.