Mawu a M'munsi
a Malemba amaphunzitsa momveka bwino kuti Yehova Mulungu ndi Mlengi. Koma anthu ambiri sakhulupirira zimenezi. Iwo amanena kuti moyo unangoyamba wokha. Zimene amanenazi sizingatisokoneze ngati timachita khama kuti tizikhulupirira kwambiri Mulungu komanso Baibulo. Nkhaniyi itithandiza kudziwa mmene tingachitire zimenezi.