Mawu a M'munsi
b M’masukulu ambiri, aphunzitsi saphunzitsa ngakhale pang’ono kuti zinthu zinachita kulengedwa. Iwo amanena kuti kuchita zimenezi kungakhale ngati kukakamiza ophunzira kuti azikhulupirira kuti kuli Mulungu.