Mawu a M'munsi
c Mungapeze mfundo zimene ananena anthu ena ophunzira kwambiri oposa 60, kuphatikizaponso asayansi omwe amakhulupirira kuti zinthu zinachita kulengedwa, mu Watch Tower Publications Index. Pamutu wakuti, “Science” pitani pamene alemba kuti “scientists expressing belief in creation.” Mfundo zina mungazipeze mu Buku la Mboni za Yehova Lofufuzira Nkhani. Pamutu wakuti “Sayansi ndi Luso la Zopangapanga,” pitani pomwe alemba kuti, “Kucheza ndi Munthu Wina.” (Nkhani za mu Galamukani!)