Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Timakonda kwambiri Yehova ndipo timafuna kuchita zonse zomwe tingathe pomutumikira. Chifukwa cha zimenezi, tingafune kuwonjezera utumiki wathu kapena kuyesetsa kuti tizitumikira m’maudindo ena mumpingo. Komabe mwina tingayesetse koma n’kulephera kukwaniritsa zolinga zomwe tili nazo. Ndiye kodi tingatani kuti tipitirize kuchita zambiri potumikira Yehova n’kumakhalabe osangalala? Tingapeze yankho la funso limeneli m’fanizo la Yesu la matalente.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena