Mawu a M'munsi
a Zinthu zina zomwe timasankha pa moyo wathu, zimakhudza nthawi komanso mphamvu zomwe tingagwiritse ntchito potumikira Yehova. Makamaka anthu amene angokwatirana kumene, amafunika kusankha zochita pa zinthu zomwe zingakhudze moyo wawo wonse. Nkhaniyi ithandiza okwatirana kuti azisankha zochita mwanzeru kuti azikhala ndi moyo wosangalala.