Mawu a M'munsi
a Kodi chikondi chokhulupirika n’chiyani? Kodi Yehova amasonyeza kwa ndani chikondi chokhulupirika? Nanga anthu amene amasonyezedwa chikondichi chimawathandiza bwanji? Nkhaniyi iyankha mafunso amenewa ndipo nkhani imeneyi komanso yotsatira zifotokoza khalidwe lofunikali.