Mawu a M'munsi
d MAWU OFOTOKOZERA ZITHUNZI: Yehova amasonyeza chikondi chake kwa anthu onse kuphatikizapo atumiki ake. Tizithunzi tomwe tili m’mwamba mwa chithunzi chosonyeza gulu la anthu, tikuonetsa mmene Mulungu amasonyezera chikondi. Njira yaikulu ndi kupereka mwayi wopindula ndi nsembe ya dipo.