Mawu a M'munsi
e MAWU OFOTOKOZERA ZITHUNZI: Kuwonjezera pa chikondi chimene amasonyeza anthu onse, anthu amene amakhala atumiki ake n’kumakhulupirira nsembe ya dipo, Yehova amawasonyeza chikondi chokhulupirika. Zina mwa njira zimene amawasonyezera chikondichi, zasonyezedwa mutizithunzi ting’onoting’ono.