Mawu a M'munsi
d Mawu a Chigiriki amene anawamasulira kuti “mnzako” pa Mateyu 22:39, sikuti amangonena za munthu amene timakhala moyandikana naye. Mawuwa anganenenso za munthu amene timachita naye zinthu.