Mawu a M'munsi
a Monga Mlengi wa zinthu zonse, Yehova ndi woyenera kulambiridwa. Zimene timachita pomulambira zimakhala zovomerezeka kwa iye, tikamamvera malamulo ake komanso kuchita zinthu mogwirizana ndi mfundo zake. Munkhaniyi tikambirana zinthu zosiyanasiyana 8, zimene timachita polambira Mulungu. Tiphunzira mmene tingamachitire bwino zinthu zimenezi kuti tizisangalala kwambiri.