Mawu a M'munsi
a Sitingamvetse bwinobwino uthenga wa m’Baibulo ngati titapanda kumvetsa ulosi wa pa Genesis 3:15. Kuphunzira ulosiwu kungalimbitse chikhulupiriro chathu mwa Yehova komanso kuti tisamakaikire ngakhale pang’ono kuti adzakwaniritsa malonjezo ake onse.