Mawu a M'munsi
a Moyo si wophweka mādzikoli. Abale ndi alongo athu akukumana ndi mavuto ambiri. Tikhoza kuwathandiza kwambiri ngati titamafufuza njira zowalimbikitsira. Pa nkhaniyi tingachite bwino kuganizira chitsanzo cha mtumwi Paulo.