Mawu a M'munsi
a Nthawi zina mafuko a Aisiraeli ankamenyana okhaokha, ngakhale kuti nkhondo zimenezi sizinkasangalatsa Yehova. (1 Maf. 12:24) Komabe nthawi zina ankalola kuti zimenezi zichitike chifukwa choti mafuko ena sanamumvere kapena achita machimo aakulu.—Ower. 20:3-35; 2 Mbiri 13:3-18; 25:14-22; 28:1-8.