Mawu a M'munsi
a Mādziko lolamuliridwa ndi Satanali, anthu ambiri si oleza mtima. Komabe, Baibulo limatiuza kuti tikhale oleza mtima. Nkhaniyi ifotokoza chifukwa chake khalidweli lili lofunika komanso zimene tingachite kuti tizikhala oleza mtima kwambiri.