Mawu a M'munsi
b Mungapeze nkhani zakuti “Mfundo Zothandiza Mabanja” pa jw.org. Nkhani zina zimene zingathandize mwamuna ndi mkazi wake zomwe zilipo ndi zakuti: “Kodi Mungasonyezane Bwanji Ulemu?” komanso “Kodi Mungasonyeze Bwanji kuti Mumayamikira Zimene Mwamuna Kapena Mkazi Wanu Amachita?” Zomwe zingathandize makolo: “Phunzitsani Ana Anu Kugwiritsa Ntchito Foni Mosamala” komanso “Zimene Mungachite Kuti Muzimasukirana ndi Mwana Wanu.” Zimene zingathandize achinyamata: “Kodi Mungatani Kuti Musamangotengera Zochita za Anzanu?” komanso “Kodi Mungatani Ngati Mumasowa Wocheza Naye?”