Mawu a M'munsi
a Mwachitsanzo, Mkhristu angakane kugwira ntchito kuti azipeza zinthu zofunika ngakhale kuti angakwanitse. Mwinanso angakakamire kuchita chibwenzi ndi wosakhulupirira kapena angamafalitse nkhani zoipa zomwe zingachititse kuti anthu asamagwirizane mwinanso miseche. (1 Akor. 7:39; 2 Akor. 6:14; 2 Ates. 3:11, 12; 1 Tim. 5:13) Anthu amene amapitiriza kuchita makhalidwe ngati amenewa, ndi ‘osalongosoka.’