Mawu a M'munsi
a M’machaputala 2 ndi 3 a kalata yake yoyamba, mtumwi Petulo anafotokoza nthawi zingapo pomwe Akhristu anachitiridwa zinthu zopanda chilungamo ndi mabwana awo ankhanza kapena amuna awo osakhulupirira.—1 Pet. 2:18-20; 3:1-6, 8, 9.