Mawu a M'munsi
a Patapita zaka ziwiri ndi hafu kuchokera pamene anakumana ndi Yesu, Nikodemo anali adakali mmodzi wa oweruza a Khoti Lalikulu la Ayuda. (Yoh. 7:45-52) Olemba mbiri ena amanena kuti Nikodemo anakhala wophunzira pambuyo poti Yesu waphedwa.—Yoh. 19:38-40.