Mawu a M'munsi
b Zikuoneka kuti Mariya wa ku Magadala anali mmodzi wa amayi amene ankayenda ndi Yesu. Amayiwa ankathandiza Yesu ndi atumwi ake pogwiritsa ntchito chuma chawo.—Mat. 27:55, 56; Luka 8:1-3.