Mawu a M'munsi
a Zikuoneka kuti mzimu woipa ndi umene unachititsa Elifazi kunena kuti Yehova saona munthu aliyense kuti ndi wolungama moti palibe amene angasangalatse Mulungu. Elifazi ankakhulupirira mfundo yabodzayi ndipo nthawi zonse akamalankhula ndi Yobu ankabwereza mfundo yolakwikayi.—Yobu 4:17; 15:15, 16; 22:2.