Mawu a M'munsi
a Kutatsala milungu ingapo kuti lamulo loletsa ntchito ya Mboni za Yehova liperekedwe, ansembe a Katolika ankalemba nkhani zitalizitali n’kumazifalitsa m’manyuzipepala. Nkhanizo zinali zonyoza a Mboni za Yehova komanso ankawanamizira kuti amagwirizana ndi oukira boma