Mawu a M'munsi
a Kwa zaka zambiri Ophunzira Baibulo ankavala kabaji kokhala ndi mtanda ndiponso chisoti chachifumu. Chizindikirochi chinkaikidwanso pa magazini a Nsanja ya Olonda. Koma pofika m’ma 1930, a Mboni za Yehova anasiya kugwiritsa ntchito chizindikirochi.