Mawu a M'munsi
a Poyamba dzikoli linkadziwikanso kuti Dutch East Indies. Pa nthawi imene abalewa ankakambirana nkhaniyi, Adatchi anali atalamulira dzikoli kwa zaka 300. Adatchiwa ankachita bizinezi yogula ndi kugulitsa zokometsera zakudya. Mânkhaniyi tigwiritsa ntchito mayina a malo omwe anthu akuwadziwa panopa.