Mawu a M'munsi
a Patapita nthawi, bambo ake a Felix ndi azing’ono awo anakhalanso a Mboni. Mchemwali wake Josephine, anakwatiwa ndi André Elias ndipo banjali linalowa Sukulu ya Giliyadi Yophunzitsa Baibulo. Nkhani yonena za moyo wa Josephine Elias ili mu September 2009.