Mawu a M'munsi
a Baibulo la Dziko Latsopano lathunthu la Chiindoneziya, linatulutsidwa mu 1999. Abale anamasulira Baibuloli pa nthawi imene ntchito yathu inali yoletsedwa ku Indonesia ndipo anagwira ntchitoyi kwa zaka 7. Patatha zaka zingapo, mavoliyumu awiri a Insight on the Scriptures ndiponso Watchtower Library ya pa CD, zinatulutsidwa mâChiindoneziya. Kunena zoona abale amenewa anagwira ntchito yotamandika zedi.